Tsamba 2
Akazi Kodi Ali ndi Tsogolo Lotani? 3-14
Kaŵirikaŵiri Akazi Sawakonda Ndipo Amawachitira Chiwawa. Koma Posachedwa Miyoyo Yawo Idzasintha.
Kodi Ziŵanda Zilipodi? 16
Kodi ziŵanda zilipodi? Kodi Baibulo limati chiyani?
[Mawu a Chithunzi patsamba 2]
ZITHUNZI ZA PACHIKUTO: Pamwamba kumanzere ndi pansi kumanja: Godo-Foto