Tsamba 2
Nkhondo Yolimbana ndi AIDS—Kodi Tidzapambana? 3-9
Kodi AIDS tingaitenge motani? Kodi nkuti kumene tsopano ili yofala? Kodi tingathe kuigonjetsa? Nkhani zoyambirira zikuyankha mafunso ameneŵa kuphatikizapo ena.
Kuzunza Nyama—Kodi Nkulakwa? 26
Ndewu ya agalu, ndewu ya atambala, ndewu ya akavalo, ndewu ya ng’ombe—kwa zaka zikwi zambiri, anthu akhala akuchitira nkhanza nyama nkumati ndi maseŵera. Kodi Baibulo limanenanji pa zimenezi?
[Mawu a Chithunzi patsamba 2]
PACHIKUTO: Chad Slattery/Tony Stone Images (Model is not associated with subject matter.)