Tsamba 2
Nyimbo N’zamphamvu Kuposa Mmene Mungaziganizire 3-10
Kodi nyimbo zingatikhudze motani? Kodi tiyenera kuonetsetsa chiyani tikamasankha zimene timamvetsera?
Mmene Mungasankhire Wokwatirana Naye 18
Kodi Baibulo limanenanji pankhani imeneyi?
Tetezani Mwana Wanu Kungozi 20
Kodi tingachepetse bwanji ngozi zimene zimakhudza ana? Kodi tingatani ngati zitachitika?
[Mawu a Chithunzi patsamba 2]
CHIKUTO: Chithunzi cha munthu akuimba chitoliro: Garo Nalbandiana