Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • g 10/06 tsamba 27-31
  • Kodi Mungayankhe Bwanji?

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • Kodi Mungayankhe Bwanji?
  • Galamukani!—2006
  • Timitu
  • Nkhani Yofanana
  • TCHULANI ZOLENGEDWA ZAUZIMUZI
  • ZINACHITIKA LITI?
  • NDINE NDANI?
  • NDINE NDANI?
  • KUCHOKERA M’MAGAZINI INO
  • Zithunzi Zoti Ana Apeze
  • MAYANKHO A MAFUNSO A PA TSAMBA 31
  • Kodi Mungayankhe Bwanji?
    Galamukani!—2007
  • Kodi Mungayankhe Bwanji?
    Galamukani!—2006
  • Kodi Mungayankhe Bwanji?
    Galamukani!—2006
  • Kodi Mungayankhe Bwanji?
    Galamukani!—2007
Onani Zambiri
Galamukani!—2006
g 10/06 tsamba 27-31

Kodi Mungayankhe Bwanji?

TCHULANI ZOLENGEDWA ZAUZIMUZI

Lembani mzere kulumikiza mtundu wa mngelo ndi chithunzi chogwirizana naye, kenaka yankhani funsolo.

Mkulu wa angelo

Kodi mkulu wa angeloyu amadziwika ndi dzina loti chiyani?

Akerubi

Kodi akerubi ankalondera chiyani mu Edene?

Aserafi

Kodi Yesaya anamva aserafi akunena chiyani?

Angelo

Kodi angelo onse pamodzi alipo osachepera angati?

1. ․․․․․

2. ․․․․․

3. ․․․․․

4. ․․․․․

◼ Kambiranani: Kodi kudziwa za banja la Yehova lakumwamba kungakuthandizeni bwanji kulimba mtima?—2 Mafumu 6:15-17.

ZINACHITIKA LITI?

Lembani mzere wolumikiza chochitika chilichonse ku chaka chomwe chinachitikira.

1761 B.C.E. Cha m’ma538 B.C.E. 33 C.E.

1728 B.C.E. Cha M’ma455 B.C.E. 44 C.E.

5. Machitidwe 12:5-11

6. Genesis 32:22-30

7. Danieli 6:22

NDINE NDANI?

8. Sindinamvere machenjezo a mngelo ndi kulira kwa bulu.

NDINE NDANI?

9. Ndinapereka uthenga kwa Danieli, Zekariya, ndi kwa mayi a Emanueli.

KUCHOKERA M’MAGAZINI INO

Yankhani mafunso awa, ndipo lembani vesi kapena mavesi a m’Baibulo omwe akusowekapo.

Tsamba 3 Kodi kuonera TV kukufanana bwanji ndi kudya uchi? (Miyambo 25:․․․)

Tsamba 7 N’chifukwa chiyani tiyenera kusamala n’zimene timaonera pa TV? (Miyambo 13:․․․)

Tsamba 11 Kodi munthu akafa maganizo ake amatani? (Salmo 146:․․․)

Tsamba 21 Kodi Yehova amaona bwanji achinyamata amene ali ndi matenda ovutika kudya? (Salmo 22:․․․)

Zithunzi Zoti Ana Apeze

Kodi mungathe kupeza zithunzi izi m’magazini ino? M’mawu anuanu, fotokozani zimene zikuchitika pa chithunzi chilichonse.

(Mayankho ali patsamba 27)

MAYANKHO A MAFUNSO A PA TSAMBA 31

1. Akerubi. “Njira ya ku mtengo wa moyo.”—Genesis 3:24.

2. Mkulu wa angelo. Mikayeli.—Yuda 9.

3. Angelo. Mamiliyoni ambiri.—Danieli 7:10.

4. Aserafi. “Woyera, Woyera, Woyera, Yehova.”—Yesaya 6:3, 6, 7.

5. 44 C.E.

6. 1761 B.C.E.

7. Cha m’ma 538 B.C.E.

8. Balamu.

9. Gabrieli.

[Mawu a Chithunzi patsamba 31]

Middle circle: ©Alan Copson/​Agency Jon Arnold Images/​age fotostock

    Mabuku a Chichewa (1974-2025)
    Tulukani
    Lowani
    • Chichewa
    • Tumizirani Ena
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • Privacy Settings
    • JW.ORG
    • Lowani
    Tumizirani Ena