Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • g 5/09 tsamba 31
  • Kodi Mungayankhe Bwanji?

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • Kodi Mungayankhe Bwanji?
  • Galamukani!—2009
  • Timitu
  • Nkhani Yofanana
  • Zinachitikira Kuti?
  • Kuchokera M’magazini Ino
  • Zithunzi Zoti Ana Apeze
  • Kodi Mumadziwa Chiyani za Aneneri?
  • Werengani Amosi 7:10-17, ndiyeno yankhani mafunso otsatirawa.
  • MAYANKHO A MAFUNSO A PATSAMBA 31
  • Kodi Mungayankhe Bwanji?
    Galamukani!—2009
  • Kodi Mungayankhe Bwanji?
    Galamukani!—2008
  • Zoti Banja Likambirane
    Galamukani!—2010
  • Kodi Mungayankhe Bwanji?
    Galamukani!—2009
Onani Zambiri
Galamukani!—2009
g 5/09 tsamba 31

Kodi Mungayankhe Bwanji?

Zinachitikira Kuti?

1. Kodi thanthwe limene Mose anamenya kuti atulutsire Aisiraeli madzi linali kuti?

ZOKUTHANDIZANI: Werengani Numeri 20:1-8.

Lembani mzere wozungulira yankho lanu pamapupo.

Kadesi

Refidimu

Phiri la Sinai (Horebe)

◼ Kodi Mose ndi Aroni analakwitsa chiyani, ndipo analandira chilango chotani?

․․․․․

ZOKUTHANDIZANI: Werengani Numeri 20:9-13; Salmo 106:32, 33.

KAMBIRANANI:

Kodi mukuganiza kuti Mose anakwiyira Aisiraeli chifukwa chiyani? N’chifukwa chiyani muyenera kupewa kupsa mtima msanga?

Kuchokera M’magazini Ino

Yankhani mafunsowa, ndipo lembani vesi kapena mavesi a m’Baibulo omwe akusowapo.

TSAMBA 7 Kodi mayanjano oipa amawononga chiyani? 1 Akorinto 15:․․․

TSAMBA 8 Kodi osangalala ndi amene amazindikira chiyani? Mateyo 5:․․․

TSAMBA 13 Kodi moyo wathu uyenera kukhala wosakonda chiyani? Aheberi 13:․․․

TSAMBA 18 Kodi chikondi sichichita chiyani? 1 Akorinto 13:․․․

Zithunzi Zoti Ana Apeze

Kodi mungathe kupeza zithunzi izi m’magazini ino? Fotokozani zimene zikuchitika pa chithunzi chilichonse.

Kodi Mumadziwa Chiyani za Aneneri?

Werengani Amosi 7:10-17, ndiyeno yankhani mafunso otsatirawa.

2. ․․․․․

Kodi wansembe Amaziya anadzudzula Amosi chifukwa chiyani?

3. ․․․․․

Kodi ndi makhalidwe awiri ati amene Amosi anasonyeza poyankha mawu achipongwe a Amaziya?

KAMBIRANANI:

Kodi mungaleke kunena za Yehova chifukwa chakuti ena akukunyozani? N’chifukwa chiyani mwayankha choncho?

◼ Mayankho ali pa tsamba 11

MAYANKHO A MAFUNSO A PATSAMBA 31

1. Kadesi.

◼ Mose analankhula mokalipa, ndipo iye ndi Aroni sanayeretse dzina la Yehova, choncho sanaloledwe kulowa Dziko Lolonjezedwa.

2. Anachitira mfumu chiwembu.

3. Kudzichepetsa ndiponso kulimba mtima.

[Mawu a Chithunzi patsamba 31]

Map: Based on maps copyrighted by Pictorial Archive (Near Eastern History) Est. and Survey of Israel

    Mabuku a Chichewa (1974-2025)
    Tulukani
    Lowani
    • Chichewa
    • Tumizirani Ena
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • Privacy Settings
    • JW.ORG
    • Lowani
    Tumizirani Ena