Zamkatimu
November 2013
© 2013 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania.
MUNGAPEZE ZAMBIRI PA WEBUSAITI YA
ACHINYAMATA
Mukhoza kupeza mayankho a m’Baibulo a mafunso ambiri omwe achinyamata amadzifunsa. Ena mwa mafunsowa ndi awa:
• “Kodi Ndimada Nkhawa Kwambiri Ndi Mmene Ndimaonekera?”
• “Kodi Ndingatani Ngati Ndikudwala Matenda Aakulu?”
• “N’chifukwa Chiyani Ndimadzivulaza?”
(Fufuzani pa mawu akuti ZIMENE BAIBULO LIMAPHUNZITSA > ACHINYAMATA)
ANA
Werengani nkhani zomwe zafotokozedwa pogwiritsa ntchito zithunzi. Gwiritsani ntchito nkhanizi kuthandizira ana anu kudziwa zambiri za anthu otchulidwa m’Baibulo komanso kuwathandiza kuti akhale ndi makhalidwe abwino.
(Fufuzani pa mawu akuti ZIMENE BAIBULO LIMAPHUNZITSA > ANA)