Mlozera Nkhani wa Magazini a Galamukani! a 2013
CHIPEMBEDZO
KUCHEZA NDI ANTHU
“Sakayikira Zoti Mulungu Analenga Zamoyo Zonse” (Schenck, B.), 4/13
Wasayansi yofufuza mmene maselo a m’thupi amagwirira ntchito (Chiozzi, P.), 1/13
MAUNANSI A ANTHU
Ngati Mumacheza Kwambiri ndi Munthu Amene si Mwamuna Kapena Mkazi Wanu, 10/13
Zimene Mungachite Kuti Musamasiye Kulankhulana Mukasemphana Maganizo, 6/13