Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • ll gawo 2 tsamba 6-7
  • Kodi Mulungu Woona Ndani?

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • Kodi Mulungu Woona Ndani?
  • Mverani Mulungu Kuti Mudzapeze Moyo Wosatha
  • Nkhani Yofanana
  • Chigawo 2
    Mverani Mulungu
  • Kodi Ndani Anakulengani?
    Sangalalani Ndi Moyo pa Dziko Lapansi Kosatha!
  • Kuyankha Mafunso a M’Baibulo
    Nsanja ya Olonda—2013
  • Kodi Anthu Akafa Amapita Kudziko la Mizimu?
    Kodi Mizimu ya Akufa Ilipodi?
Onani Zambiri
Mverani Mulungu Kuti Mudzapeze Moyo Wosatha
ll gawo 2 tsamba 6-7

CHIGAWO 2

Kodi Mulungu Woona Ndani?

Yehova ali pampando wake wachifumu ndipo akuyang’ana zolengedwa zake zakumwamba komanso zapadziko lapansi

Pali Mulungu woona mmodzi yekha ndipo dzina lake ndi Yehova. (Salimo 83:18) Iye ndi Mzimu ndipo sitingathe kumuona. Iye amatikonda ndipo amafuna kuti ifenso tizimukonda komanso tizikonda anthu anzathu. (Mateyu 22:35-40) Iye ndi Wamkulukulu ndiponso ndi Mlengi wa zinthu zonse.

Poyambirira Mulungu analenga munthu wauzimu wamphamvu kwambiri amene kenako anadzatchedwa Yesu Khristu. Komanso Yehova analenga angelo.

Yehova analenga zinthu zonse zakumwamba . . . ndi zapadziko lapansi. Chivumbulutso 4:11

Yehova Mulungu analenga nyenyezi, dziko lapansi ndi zonse zimene zili padzikoli.​—Genesis 1:1.

Anaumba Adamu, munthu woyamba, kuchokera kufumbi lapansi.​—Genesis 2:7.

  • N’chifukwa chiyani tiyenera kulemekeza Yehova?​—Yesaya 42:5.

  • Kodi ena mwa makhalidwe a Mulungu ndi ati?​—Ekisodo 34:6.

    Mabuku a Chichewa (1974-2025)
    Tulukani
    Lowani
    • Chichewa
    • Tumizirani Ena
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • Privacy Settings
    • JW.ORG
    • Lowani
    Tumizirani Ena