Chosonyezera Nkhani za mu Nsanja ya Olonda za 1987
Chosonyeza deti la kope m’limene nkhaniyo ikupezeka
CHIDZIŴITSO PA NYUZI
1/15, 6/15, 10/15
MAFUNSO OCHOKERA KWA OŴERENGA
“Bukhu la moyo la Mulungu,” 9/1
Cholakwa cha Mose, 10/15
“Dziko latsopano”? 5/1
Kukwatiranso mnzanu wa mu ukwati pa chiwukiriro? 6/1
Kulira kwa Yesu ‘mwandisiiranji?’ 6/15
Kupenda thupi, 4/1
Malaki 2:15, 9/15
Miyambo 30:4, 7/15
Nchifukwa ninji mtembenuki wa Afarisi anasandutsidwa mwana wa Gehena? 10/1
Ngamira kapena chingwe kupyola diso la singano? 12/1
“Zinthu zovumbulutsidwa” (Deut. 29:29), 5/15
MBIRI YA MOYO WA MUNTHU
‘Chikho Changa Chasefukira’ (T. Gott), 6/1
Kukhala Moyandikira ku gulu la Yehova (J. Barr), 7/1
Kuyang’ana M’mbuyo Kuposa Zaka 93 za Kukhala ndi Moyo (F. W. Franz), 5/1
Mbadwo Wanga—Wapadera ndi wa Mwaŵi Wapamwamba (M. Sargent), 8/1
Ndawona Kuti Yehova Ali Wabwino (L. Johnson), 10/1
Yehova Akutichinjiriza (E. Kattner), 4/1
MBONI ZA YEHOVA
“Achangu Kaamba ka Ntchito Zabwino” mu Kenya, 4/15
Chikondwerero Pakati pa Anthu a Mulungu, 1/1
Chiwonjezeko Chabwino “Kuseri kwa Mapiri” (Haiti), 11/1
Chiwonjezeko mu Gibraltar, 10/15
“Chokumana Nacho Cholemera,” 4/1
Chokwaniritsa Chozizwitsa cha Costa Rica, 9/1
Dziko la Zinenero 700 (Papua New Guinea), 9/15
Kuitana kwa Zisumbu za Micronesia, 11/15
Kukhulupirika kwa Chikristu mu New Caledonia, 8/15
Kumaliza Maphunziro kwa Gileadi, 6/1, 12/1
M’munda wa Umishonale, 1/15
Mphatso Yapadera ya Ana, 8/1
Msonkhano wa Chigawo wa “Khulupirirani Yehova,” 2/1
Sukulu Yatsopano Yodzatsegulidwa! 6/1
Ufulu wa Chipembedzo Usungidwa mu India, 11/1
Yehova Amanga Nyumba (South Africa), 12/15
MFUNDO ZAZIKULU ZA BAIBULO
Miyambo, 5/15
Mlaliki, 9/15
Nyimbo ya Solomo, 11/15
MOYO NDI UMINISITALA ZA YESU
(Nkhani zowoneka m’kope lirilonse.)
MOYO WACHIKRISTU NDI MIKHALIDWE
Akazi M’malo a Ntchito, 3/15
Anthu Achimwemwe—Nchifukwa Ninji? 3/15
Chikhulupiriro Chingasunthe Mapiri! 7/15
Chikristu Chowona Chimatulutsa Akristu Opanda Maziko? 7/15
Kodi Kupatsa Kwanu Kuli Nsembe? 12/1
Kodi Miyambo Imalamulira Moyo Wanu? 2/1
Kodi Mudzamamatira ku Chowonadi? 3/15
Kodi Nthaŵi Zonse Mumagwira Nsonga? 4/1
Kuchita ndi Mkwiyo, 7/1
Kusamalira Banja—Kodi Kumafutukuka Kufika ku Utali Wotani? 6/15
Kusamalira Okalamba, 6/1
Kuthandiza Mwana Kuti Akule mu Nzeru ya Umulungu, 12/15
Mankhwala a Mwambo mu Africa, 4/15
Mmene Mungapangire Mabwenzi Owona, 9/15
‘Mulungu Adzatsiriza Kuphunzitsidwa Kwanu,’ 6/15
“Nthaŵi Yolankhula—Liti? 9/1
Phindu la Kuimba M’kulambira Kowona, 12/1
Thandizo M’kupanga Zosankha za Nzeru, 5/15
Zakumwa Zoledzeretsa, 8/1
NKHANI ZAZIKULU ZOPHUNZIRIDWA
Achichepere—Kodi Mudzachitanji ndi Moyo Wanu? 8/15
Achichepere—Kodi Mukupita Patsogolo Mwauzimu? 8/15
Achimwemwe ali Awo Amene Amagwiritsira Ntchito Mphamvu Moyenera, 3/1
Ana Amene Amakondweretsa Mtima wa Yehova, 12/15
Ana—Musanyengedwe, 12/15
Chaka Choliza Lipenga cha Akristu Chifika pa Chimake mu Zaka Chikwi, 1/1
Chaka Choliza Lipenga cha Yehova—Nthaŵi Yathu ya Kusangalala, 1/1
Chenjerani ndi Kugwiritsira Ntchito Molakwika Mphamvu, 3/1
Chilango Chimabala Chipatso cha Mtendere, 10/1
Chisungiko cha Dziko Lonse Pansi pa “Kalonga wa Mtendere,” 4/1
Dziko Lapansi Silinayenera Iwo, 1/15
“Ine Ndiimabe Pamwamba pa Nsanja,” 3/1
Khulupirirani Yehova—Osati mu “Chiwembu!” 9/1
Kodi Mapemphero Anu Ali Atanthauzo Motani? 7/15
Kodi Mudzanena Kuti, “Ndine Pano! Munditumize Ine”? 10/15
Kodi Mukukhalabe Osadetsedwa M’njira Iriyonse? 11/1
Kodi Muli Okhutiritsidwa ndi Makonzedwe Auzimu a Yehova? 10/1
Kristu Mokangalika Akutsogolera Mpingo Wake, 8/1
Kubadwa kwa Mwana Kwakukulu Koposa kwa Padziko Lapansi Kutsogolera ku Chisungiko cha Dziko Lonse, 4/1
Kugwirizana ndi Osunga Umphumphu a Yehova, 1/1
Kukhala Ogalamuka Molimbana ndi “Mtendere ndi Chisungiko” Monga Kwaganiziridwa ndi Mitundu, 9/1
Kulemekeza Mulungu wa Chiyembekezo, 12/15
Kulungamitsa Zinthu Pakati pa Mulungu ndi Inu, 10/15
Kumachita Mmene Tingathere Kulalikira Mbiri Yabwino, 2/1
Kumamvera Yehova Pamene Mapeto Akuyandikira, 5/15
Kumayang’anitsitsa pa Zikondwerero za Okalamba, 6/1
‘Kumayenda M’njira ya Chowonadi,’ 3/1
Kupanga Zinthu Zonse Kukhala Zatsopano, 3/1
Kupeza Mtendere ndi Mulungu mwa Kudzipereka ndi Ubatizo, 4/15
Kuphunzira Kupembedza Mulungu Kulinga kwa Makolo Okalamba, 6/1
Kupulumutsa Moyo M’nthawi ya Njala, 5/1
Kupuma “Mpweya” wa Dziko Lino Kuli Kwakupha! 9/15
Kusonyeza Chiyamikiro Kaamba ka Zisonyezero Ziŵiri Zazikulu Kwambiri za Chikondi, 12/15
Kuwopa Mulungu—Kodi Kungakupindulitseni? 12/1
Kuyesedwa ndi Kusefedwa M’nthaŵi Zamakono, 6/15
Lankhulani Ponena za Ulemelero wa Ufumu wa Mulungu, 10/15
Madalitso Aumulungu kwa “Awo Okhala ndi Chidziŵitso,” 7/1
Mapemphero Amafunikira Zintchito, 7/15
Mikayeli Kalonga Wamkulu Aimirira, 7/1
Mmene Mungakumanire ndi Mtendere Waumulungu Mokwanira Kwambiri, 3/15
Mtambo Waukulu Wotere wa Mboni! 1/15
Mtendere Potsirizira!—Pamene Mulungu Alankhula, 5/15
Mtendere Waumulungu Kaamba ka Awo Ophunzitsidwa ndi Yehova, 3/15
“Muzikhala Oyera Mtima . . . ” 11/1
Njala Yopatsa Imfa mu Nthaŵi ya Mwana Alirenji, 5/1
Nthaŵi ya Kuyesedwa ndi Kusefedwa, 6/15
Onjezerani Mtendere Wanu Mwachidziŵitso Cholongosoka, 4/15
‘Palibe Mtendere kwa Oipa,’ 7/1
Pitirizani Kugonjera ku “Mzimu Womwe Uli Wopatsa Moyo,” 9/15
Pitirizani Kukhala ndi Moyo Monga Ana a Mulungu, 2/1
Pitirizani Kuyenda M’kuwunika kwa Umulungu, 1/15
Sungani Kuwopa Kwanu Yehova, 12/1
Sonyezani Chikondi ndi Chikhulupiriro Nthaŵi Zonse, 2/1
Sonyezani Kufunitsitsa ku Kulalikira Mbiri Yabwino, 2/1
Umbeta—Njira Yopatsa Mphoto ya Moyo, 11/15
Utsogoleri Wokangalika wa Kristu Lerolino, 8/1
Wosakwatira koma Wokwanira Kaamba ka Utumiki wa Mulungu, 11/15
Yembekeza Yehova, 12/15
Zisonyezero Ziŵiri Zazikulu Kwambiri za Chikondi, 12/15
NKHANI ZOSIYANASIYANA
Anabaptists, 11/15
Angelo—Amayambukira Moyo Wanu? 12/15
Baibulo la William Tyndale, 7/15
Chifuno cha Ulosi, 5/1
Chipembedzo Chingakhutiritse Zosowa Zathu? 11/15
Chipembedzo Mphamvu ya Makhalidwe Abwino? 10/15
Funde Lalikulu la Chipembedzo—Chiitano Chomalizira, 11/1
Kodi Chipembedzo Chamakono Chiri Chogwira Ntchito Motani? 10/1
Kodi Miyendo Yake Inali Kuti? 8/15
Kodi Mtanda uli wa Akristu? 8/15
Kuchiritsa kwa Chikhulupiriro—Kuchokera kwa Mulungu? 12/1
Kuchita Ulauli, 3/1
Kuchokera ku Ukapolo Wopanga Njerwa Kupita ku Ufulu! 11/15
Kukhulupirira Malaulo, 11/1
Kukhulupirira Mizimu—Kumawonedwa Motani ndi Mulungu? 9/1
Kunyalanyaza Machenjezo ndi Kuyesa Mulungu, 12/15
Kuwopsya kwa Chuma ndi Umphaŵi, 9/15
Lalikirani Ufulu! 1/1
Madzi Akukonzanso Aphulika, 10/1
Maulosi Onse Amachokera kwa Mulungu? 5/1
Mbali Yowongoleredwa ya Akazi, 8/15
Mbiri ya Chipembedzo iri ya Phindu Lirilonse? 9/15
Mumadera Nkhaŵa Ponena za Ana Anu? 12/15
“Utatu Wodalitsidwa”—Kodi Uli mu Baibulo? 6/15
Uthenga wa Mayanjano, 1/15
RIPOTI LA OLENGEZA UFUMU
(M’kope lirilonse la 1 la mwezi.)
YEHOVA
Kodi Mulungu Ali Munthu Weniweni? 4/1
Kodi Nchiyani Chimene Mulungu Wachita Kaamba ka Inu? 5/15
Nzeru ya Mulungu Kodi Mukuiwona Iyo? 4/15
Wokhalako Wamkulukulu Ali Wapadera, 6/15