Zamkatimu
August 15, 2012
© 2012 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania. Ulamuliro wonse pa magazini ino ndi wathu.
Magazini Yophunzira
NKHANI ZOPHUNZIRA
SEPTEMBER 24-30, 2012
TSAMBA 3 • NYIMBO: 65, 2
OCTOBER 1-7, 2012
Muzichita Zinthu Monga Nzika za Ufumu
TSAMBA 11 • NYIMBO: 16, 98
OCTOBER 8-14, 2012
Samalani ndi Misampha ya Mdyerekezi
TSAMBA 20 • NYIMBO: 61, 25
OCTOBER 15-21, 2012
Musasunthike Popewa Misampha ya Satana
TSAMBA 25 • NYIMBO: 32, 83
CHOLINGA CHA NKHANI ZOPHUNZIRA
NKHANI YOPHUNZIRA 1 TSAMBA 3-7
Danieli analosera kuti “nthawi yamapeto,” anthu ambiri adzadziwa “zinthu zambiri zoona.” (Dan. 12:4) Nkhaniyi ikufotokoza za kukwaniritsidwa kwa ulosiwu. Ikufotokozanso umboni wosonyeza kuti Yesu akuthandiza anthu amene akutumikira Yehova Mulungu.
NKHANI YOPHUNZIRA 2 TSAMBA 11-15
Nkhaniyi ikuthandizani kudziwa nzika za Ufumu. Ikufotokoza zimene anthu ayenera kuchita kuti akhale nzika. Ikufotokozanso mmene nzikazo zingasonyezere kuti zimakonda malamulo a Yehova.
NKHANI ZOPHUNZIRA 3, 4 TSAMBA 20-29
Satana amagwiritsa ntchito misampha mochenjera kuti asokoneze chikhulupiriro chathu. Nkhanizi zikufotokoza mmene tingadzitetezere ku misampha isanu. Misamphayo ndi kusalankhula bwino, kuopa anthu ndiponso kufuna kuwasangalatsa, kudziimba mlandu kwambiri, kukonda chuma ndiponso chigololo.
M’MAGAZINI INO MULINSO NKHANI IZI
8 “Mudzapeza Mphoto Chifukwa cha Ntchito Yanu”
16 Palidi Mgwirizano Ndiponso Mapulani Abwino
31 Kale Lathu
PATSAMBA LOYAMBA: Wofalitsa akulalikira m’busa kudera lotchedwa Bafatá ku Guinea-Bissau
GUINEA-BISSAU
KULI ANTHU
1,515,000
KULI OFALITSA
120
MAPHUNZIRO A BAIBULO
389