Mawu Oyamba
Kodi Mukuganiza Bwanji?
Ngati Baibulo si buku lochokera kwa Mulungu, kodi likanapulumuka m’zinthu zonsezi?
Baibulo limanena kuti: “Udzu wobiriwirawo wauma. Maluwawo afota. Koma mawu a Mulungu wathu adzakhala mpaka kalekale.”—Yesaya 40:8.
Nkhanizi zikufotokoza mfundo zochititsa chidwi zokhudza mmene Baibulo linapulumukira m’zinthu zosiyanasiyana.