Mbiri Yateokrase
Ghana: Chiŵerengero chatsopano chapamwamba cha ofalitsa 55,539 chinachitira lipoti m’April—chiwonjezeko cha 9 peresenti pa avareji ya chaka chatha. Oposa 200,000 anafika pa Chikumbutso.
Malawi: Tsopano muli mipingo yoposa 600. Ichi ndi chiwonjezeko cha 50 peresenti pa chiŵerengero cha mipingo yomwe inalipo panthaŵi yomwe choonadi chinkatsekedwa mu October 1967.