Onani Tsamba Lomaliza
Tsamba lomaliza la chiyani? La Utumiki Wathu wa Ufumu wa m’mbuyomo. Kuti muone zitsanzo za mmene tingagaŵire mabulosha osiyanasiyana amene agaŵidwe muutumiki wa mwezi uno ndi wamaŵa, onani Utumiki Wathu wa Ufumu wa July ndi August 1995, 1996, 1997 ndi 1998.