Ndandanda ya Mlungu wa November 1
MLUNGU WOYAMBIRA NOVEMBER 1
□ Phunziro la Baibulo la Mpingo:
lv mutu 14 ndime10-14 ndi bokosi patsamba 164-165, Zakumapeto 222-223a
□ Sukulu ya Utumiki wa Mulungu:
Kuwerenga Baibulo: 1 Mbiri 16–20
Na. 1: 1 Mbiri 17:1-10
Na. 2: Kodi Zipembedzo Zina Zimatsatira Baibulo? (rs tsa. 275 ndime 3)
Na. 3: _Zinthu Zimene Malemba Amati Akhristu Oona Ayenera Kuzithawa
□ Msonkhano wa Utumiki:
Mph. 5: Zilengezo.
Mph. 10: Timapirira Mayesero Osiyanasiyana. Nkhani yochokera m’buku la Gulu, tsamba 176, ndime 2, mpaka tsamba 178, ndime 2. Funsani mwachidule wofalitsa wina kuti afotokoze chimene chimamuthandiza kupitirizabe kukhala wachangu mu utumiki ngakhale kuti ali ndi mavuto aakulu okhudza thanzi lake.
Mph. 10: Zosowa za pampingo.
Mph. 10: Konzekerani Kugawira Magazini M’mwezi wa November. Nkhani yokambirana ndi omvera. Fotokozani zimene zili m’magaziniwo kwa mphindi imodzi kapena ziwiri. Kenako sankhani mitu iwiri kapena itatu, ndipo funsani omvera kuti afotokoze mafunso ndiponso malemba amene akhoza kugwiritsa ntchito pogawira magaziniwo. Chitani chitsanzo chosonyeza mmene mungagawire magazini iliyonse.
[Mawu a M’munsi]
a Mungasankhe kukambirana bokosi kapena ayi.