Ndandanda ya Mlungu wa January 3
MLUNGU WOYAMBIRA JANUARY 3
□ Phunziro la Baibulo la Mpingo:
□ Sukulu ya Utumiki wa Mulungu:
Kuwerenga Baibulo: 2 Mbiri 29-32
Na. 1: 2 Mbiri 30:13-22
Na. 2: Kodi Yesu Khristu Anali Munthu Wabwino Chabe? (rs tsa. 424 ndime 2)
Na. 3: Mmene Anthu Amakhalira mu Ukapolo Chifukwa Choopa Imfa (Aheb. 2:15)
□ Msonkhano wa Utumiki:
Mph. 5: Zilengezo.
Mph. 10: Zosowa za pampingo.
Mph. 10: Tinapatulidwa Kuti Tichite Chifuniro Cha Yehova. Nkhani yochokera m’buku la Gulu, tsamba 168, ndime 2 mpaka kumapeto kwa mutuwo.
Mph. 10: Muzilankhula Mwachibadwa Polalikira. Nkhani yokambirana yochokera m’buku la Sukulu ya Utumiki, tsamba 128, ndime 1 mpaka tsamba 129 ndime 1. Mwachidule funsani wofalitsa waluso amene poyamba anali wamanyazi. N’chiyani chimamuthandiza kuti asamachite mantha kwambiri mu utumiki?