Ndandanda ya Mlungu wa February 13
MLUNGU WOYAMBIRA FEBRUARY 13
Nyimbo Na. 116 ndi Pemphero
□ Phunziro la Baibulo la Mpingo:
bt mutu 2 ndime 1-7 ndi bokosi patsamba 13 (Mph. 25)
□ Sukulu ya Utumiki wa Mulungu:
Kuwerenga Baibulo: Yesaya 52-57 (Mph. 10)
Na. 1: Yesaya 56:1-12 (Osapitirira mph. 4)
Na. 2: Kodi Tikuphunzira Chiyani pa Kukhulupirika kwa Petulo?—Yoh. 6:68, 69 (Mph. 5)
Na. 3: Kodi Baibulo Limaloleza Mitala?—rs tsa. 384 ndime 3–tsa. 385 ndime 3 (Mph. 5)
□ Msonkhano wa Utumiki:
Mph. 5: Zilengezo.
Mph. 10: Chifukwa Chimene Timaperekera Lipoti la Utumiki Wakumunda. Nkhani yokambidwa ndi mlembi, yochokera m’buku la Gulu, tsamba 88 ndime 1 mpaka tsamba 90 ndime 1.
Mph. 10: Kulitsani Luso la Kuphunzitsa—Gawo 1. Nkhani yochokera m’buku la Sukulu ya Utumiki, tsamba 56 ndime 1 mpaka tsamba 57 ndime 2.
Mph. 10: “Konzekerani Panopo Kuwonjezera Utumiki Wanu.” Mafunso ndi mayankho. Mukamakambirana ndime 3, pemphani woyang’anira utumiki kuti afotokoze za misonkhano yokonzekera utumiki wakumunda imene mpingo wakonza m’miyezi ya March, April ndi May.
Nyimbo Na. 107 ndi Pemphero