Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • km 10/12 tsamba 8
  • Ndandanda ya Mlungu wa November 5

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • Ndandanda ya Mlungu wa November 5
  • Utumiki Wathu wa Ufumu—2012
  • Timitu
  • MLUNGU WOYAMBIRA NOVEMBER 5
Utumiki Wathu wa Ufumu—2012
km 10/12 tsamba 8

Ndandanda ya Mlungu wa November 5

MLUNGU WOYAMBIRA NOVEMBER 5

Nyimbo Na. 123 ndi Pemphero

□ Phunziro la Baibulo la Mpingo:

bt mutu 14 ndime 11-20 (Mph. 30)

□ Sukulu ya Utumiki wa Mulungu:

Kuwerenga Baibulo: Yoweli 1-3 (Mph. 10)

Na. 1: Yoweli 2:17-27 (Osapitirira mph. 4)

Na. 2: Kodi Tingagwiritse Ntchito Bwanji Mfundo ya pa Miyambo 22:3? (Mph. 5)

Na. 3: Kodi Tingasonyeze Bwanji Kuti Timalemekeza Gulu la Yehova?—rs tsa. 143 ndime 8-12 (Mph. 5)

□ Msonkhano wa Utumiki:

Nyimbo Na. 86

Mph. 10: Akazi Amene Akulengeza Uthenga Wabwino Ndi Khamu Lalikulu. (Sal. 68:11) Nkhani yokambirana yochokera mu Nsanja ya Olonda ya September 1, 2012, tsamba 23. Yamikirani alongo onse chifukwa cha khama lawo pa ntchito yolalikira.

Mph. 10: Zosowa za pampingo.

Mph. 10: Zimene Munganene Pogawira Magazini mu November. Nkhani yokambirana. Kwa masekondi 30 kapena 60, fotokozani chifukwa chake magaziniwo angakhale othandiza m’gawo lanu. Kenako, pogwiritsa ntchito nkhani zoyambirira za mu Nsanja ya Olonda, pemphani omvera kuti anene funso lochititsa chidwi ndiponso lemba limene angawerenge pogawira magaziniwo. Chitaninso chimodzimodzi ndi nkhani zoyambirira m’magazini ya Galamukani! Ngati nthawi ilipo mungachitenso zimenezi ndi nkhani ina imodzi m’magazini ya Nsanja ya Olonda kapena Galamukani! Chitani chitsanzo chosonyeza mmene mungagawirire magazini iliyonse.

Nyimbo Na. 105 ndi Pemphero

    Mabuku a Chichewa (1974-2025)
    Tulukani
    Lowani
    • Chichewa
    • Tumizirani Ena
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • Privacy Settings
    • JW.ORG
    • Lowani
    Tumizirani Ena