Ndandanda ya Mlungu wa December 23
MLUNGU WOYAMBIRA DECEMBER 23
Nyimbo Na. 106 ndi Pemphero
□ Phunziro la Baibulo la Mpingo:
jr mutu 5 ndime 7-12 (Mph. 30)
□ Sukulu ya Utumiki wa Mulungu:
Kuwerenga Baibulo: Chivumbulutso 7-14 (Mph. 10)
Na. 1: Chivumbulutso 9:1-21 (Osapitirira mph. 4)
Na. 2: Kodi Akhristu Angasonyeze Bwanji Kuti Ndi Ochereza?—Aheb. 13:2 (Mph. 5)
Na. 3: Akhristu a mu Chipembedzo Choona Amakondana Komanso Sakhala Mbali ya Dziko—rs tsa. 90 ndime 2-3 (Mph. 5)
□ Msonkhano wa Utumiki:
Mph. 10: Mabuku Ogawira mu January ndi February. Nkhani yokambirana. Fotokozani zimene zili m’mabukuwo ndipo chitani zitsanzo ziwiri zosonyeza mmene tingawagawirire.
Mph. 20: “Kodi Tingawathandize Bwanji?” Mafunso ndi mayankho. Chitani chitsanzo chimodzi pogwiritsa ntchito mfundo zimene zili patsamba 6.
Nyimbo Na. 46 ndi Pemphero