Zilengezo
Mabuku ogawira mu October: Magazini a Nsanja ya Olonda ndi Galamukani! November ndi December: Buku lakuti, Kodi Baibulo Limaphunzitsa Chiyani Kwenikweni? kapena timapepala tatsopano. January ndi February 2016: Kabuku kakuti, Mverani Mulungu, Mverani Mulungu Kuti Mudzapeze Moyo Wosatha, Mungathe kukhala Bwenzi la Mulungu ndi kakuti, Uthenga Wabwino Wochokera kwa Mulungu.