October Ndandanda ya Mlungu wa October 12 Kuwonjezera Luso Lathu mu Utumiki—Muziphunzitsa Anthu Amene Mumaphunzira Nawo Baibulo Kuti Azikonda Kuphunzira Paokha Ndandanda ya Mlungu wa October 19 Kodi Tingatani Kuti Tiziwafika pa Mtima Anthu Amene Timaphunzira Nawo? Ndandanda ya Mlungu wa October 26 Kubwereza za M’Sukulu ya Utumiki wa Mulungu Kodi Mungatani Kuti Mawu a Mulungu Azikuthandizani pa Moyo Wanu? Ndandanda ya Mlungu wa November 2 Zilengezo Zitsanzo za Ulaliki Zochitika mu Utumiki Wakumunda