Ndandanda ya Mlungu wa December 14
MLUNGU WOYAMBIRA DECEMBER 14
Nyimbo Na. 18 ndi Pemphero
Phunziro la Baibulo la Mpingo:
cl mutu 23 ndime 1-9, ndiponso Gawo 4, patsamba 229 (30 min.)
Sukulu ya Utumiki wa Mulungu:
Kuwerenga Baibulo: 2 Mbiri 15-19 (8 min.)
Na. 1: 2 Mbiri 16:1-9 (Osapitirira 3 min.)
Na. 2: Tikuphunzira Chiyani kwa Hana pa Nkhani ya Pemphero?—ia tsa. 55 ndime 11-14 (5 min.)
Na. 3: Tiziganizira Ubwenzi Wathu Ndi Mulungu Posankha Zochita—lv tsa. 66-69 ndime 12-15 (5 min.)
Msonkhano wa Utumiki:
Mutu wa Mwezu Uno: “Tiyenera kukumana ndi masautso ambiri kuti tikalowe mu Ufumu wa Mulungu.”—Mac. 14:22.
30 min: “Yendani mwa Chikhulupiriro, Osati mwa Zooneka ndi Maso.” Mafunso ndi mayankho. M’mawu anu oyamba mugwiritse ntchito mfundo za m’ndime yoyamba ndipo pomaliza mugwiritse ntchito mfundo za m’ndime yomaliza. Ngati anthu ambiri mu mpingo wanu sangathe kuonera vidiyoyi mukambirane mfundo za mu Nsanja ya Olonda ya April 15, 2012 tsamba 25 ndi 26 ndime 13 mpaka 16.
Nyimbo Na. 133 ndi Pemphero