Ndandanda ya Mlungu wa December 21
MLUNGU WOYAMBIRA DECEMBER 21
Nyimbo Na. 3 ndi Pemphero
Phunziro la Baibulo la Mpingo:
cl mutu 23 ndime 10-18 (30 min.)
Sukulu ya Utumiki wa Mulungu:
Kuwerenga Baibulo: 2 Mbiri 20-24 (8 min.)
Na. 1: 2 Mbiri 20:13-20 (Osapitirira 3 min.)
Na. 2: Kodi Kukongola Kwenikweni Kumadziwika Bwanji?—ia tsa. 127 ndime 7-9 (5 min.)
Na. 3: Kodi Holide ya Khirisimasi Ndi Yochokera M’Baibulo?—bh tsa. 156-158 ndime 6-10 (5 min.)
Msonkhano wa Utumiki:
Mutu wa Mwezu Uno: “Tiyenera kukumana ndi masautso ambiri kuti tikalowe mu Ufumu wa Mulungu.”—Mac. 14:22.
5 min: Bokosi la Mafunso. Nkhani.
10 min: Tiziyamikira Zimene Yehova Amatipatsa. Nkhani yokambidwa ndi mkulu yochokera mu Nsanja ya Olonda ya November 15, 2015, tsamba 14 ndi 15.
15 min: Khalani Ochenjera Ngati Njoka Koma Oona Mtima Ngati Nkhunda. (Mat. 10:16) Nkhani yokambirana yochokera mu Buku Lapachaka la 2015, tsamba 73 komanso tsamba 110 mpaka 116. Pemphani omvera kuti anene zimene tikuphunzirapo.
Nyimbo Na. 137 ndi Pemphero