MOYO WATHU WACHIKHRISTU
Muzikhala Okhulupirika Wachibale Wanu Akachotsedwa
Onerani vidiyo yakuti Muzitsatira Mokhulupirika Mfundo za Yehova—Muzipewa Kuchita Zinthu ndi Anthu Ochotsedwa (imapezeka pamene palembedwa kuti BAIBULO), kenako yankhani mafunso otsatirawa:
Kodi makolo a Sonia anakumana ndi vuto lotani lomwe likanachititsa kuti asakhale okhulupirika kwa Mulungu?
Kodi n’chiyani chinawathandiza kuti akhalebe okhulupirika?
Kodi kukhulupirika kwawo kwa Yehova kunathandiza bwanji Sonia?