Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • mwb17 September tsamba 6
  • September 25–October 1

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • September 25–October 1
  • Utumiki Komanso Moyo Wathu wa Chikhristu—Ndandanda ya Misonkhano—2017
Utumiki Komanso Moyo Wathu wa Chikhristu—Ndandanda ya Misonkhano—2017
mwb17 September tsamba 6

September 25–October 1

DANIELI 4-6

  • Nyimbo Na. 67 ndi Pemphero

  • Mawu Oyamba (Osapitirira 3 min.)

CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

  • “Kodi Mupitiriza kutumikira Yehova Mosalekeza?”: (10 min.)

    • Dan. 6:7-10​—Danieli anaika moyo wake pangozi n’cholinga choti atumikire Yehova mosalekeza (w10 11/15 6 ¶16; w06 11/1 24 ¶12)

    • Dan. 6:16, 20​—Mfumu Dariyo inazindikira kuti Danieli anali pa ubwenzi wolimba ndi Yehova (w03 9/15 15 ¶2)

    • Dan. 6:22, 23​—Yehova anadalitsa Danieli chifukwa chomulambira molimba mtima (w10 2/15 18 ¶15)

  • Kufufuza Mfundo Zothandiza: (8 min.)

    • Dan. 4:10, 11, 20-22​—Kodi mtengo waukulu womwe Nebukadinezara analota unkaimira chiyani? (w07 9/1 18 ¶4)

    • Dan. 5:17, 29​—N’chifukwa chiyani poyamba Danieli anakana mphatso kuchokera kwa mfumu Belisazara koma pambuyo pake n’kulandira? (w88 10/1 30 ¶3-5; dp 109 ¶22)

    • Kodi mwaphunzira zotani zokhudza Yehova pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno?

    • Kodi ndi mfundo zina ziti zothandiza zimene mwapeza pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno?

  • Kuwerenga Baibulo: (Osapitirira 4 min.) Dan. 4:29-37

KUPHUNZITSA MWALUSO MU UTUMIKI

  • Ulendo Woyamba: (Osapitirira 2 min.) inv

  • Ulendo Wobwereza: (Osapitirira 4 min.) inv​—Sonyezani mmene mungapangire ulendo wobwereza pogwiritsa ntchito kapepala koitanira anthu kumisonkhano kamene munagawira pa ulendo woyamba.

  • Phunziro la Baibulo: (Osapitirira 6 min.) bhs 129 ¶16​—Limbikitsani wophunzira kuti azikhalabe wokhulupirika ngakhale pamene achibale ake akumutsutsa.

MOYO WATHU WACHIKHRISTU

  • Nyimbo Na. 139

  • “Muziwaphunzitsa Kuti Azitumikira Yehova Mosalekeza”: (15 min.) Nkhani yokambirana. Kenako onetsani ndiponso kukambirana vidiyo imene ikusonyeza wofalitsa waluso ali mu utumiki ndi wofalitsa watsopano.

  • Phunziro la Baibulo la Mpingo: (30 min.) kr mutu  7 ¶10-18, komanso tsamba 73

  • Mfundo Zimene Taphunzira Komanso za Mlungu Wamawa (3 min.)

  • Nyimbo Na. 73 ndi Pemphero

    Mabuku a Chichewa (1974-2025)
    Tulukani
    Lowani
    • Chichewa
    • Tumizirani Ena
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • Privacy Settings
    • JW.ORG
    • Lowani
    Tumizirani Ena