CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU | DANIELI 4-6
Kodi Mupitiriza Kutumikira Yehova Mosalekeza?
Danieli ankachita zinthu zonse zokhudza kulambira kuphatikizaponso kupemphera. Sanalole chilichonse ngakhale lamulo la mfumu, kumulepheretsa kuchita zimenezi
Kuchita zinthu zonse zokhudza kulambira kumaphatikizapo