January 21-27
MACHITIDWE 25-26
Nyimbo Na. 73 ndi Pemphero
Mawu Oyamba (Osapitirira 3 min.)
CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU
“Paulo Anapempha Kukaonekera kwa Kaisara Ndipo Kenako Analalikira Mfumu Herode Agiripa”: (10 min.)
Mac. 25:11—Paulo anagwiritsa ntchito ufulu wake ndipo anapempha kukaonekera kwa Kaisara (bt 198 ¶6)
Mac. 26:1-3—Paulo anaikira kumbuyo choonadi pamaso pa Mfumu Herode Agiripa (bt 198-201 ¶10-16)
Mac. 26:28—Mfumu Agiripa inakhudzidwa kwambiri ndi zimene Paulo ananena (bt 202 ¶18)
Kufufuza Mfundo Zothandiza: (8 min.)
Mac. 26:14—Kodi chisonga chotosera n’chiyani? (“nyama imene ikuponya miyendo yake kuti imenye zisonga zotosera” mfundo zimene ndikuphunzira pa Mac. 26:14, nwtsty; matanthauzo a mawu ena, “Chisonga chotosera” nwt)
Mac. 26:27—N’chifukwa chiyani Mfumu Agiripa inakanika kuyankha pamene Paulo anafunsa ngati imakhulupirira mwa aneneri? (w03 11/15 16-17 ¶14)
Kodi mwaphunzira zotani zokhudza Yehova pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno?
Kodi ndi mfundo zina ziti zothandiza zimene mwapeza pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno?
Kuwerenga Baibulo: (Osapitirira 4 min.) Mac. 25:1-12 (th phunziro 5)
KUPHUNZITSA MWALUSO MU UTUMIKI
Vidiyo ya Ulendo Wobwereza Woyamba: (5 min.) Onerani ndi kukambirana mfundo za m’vidiyoyi.
Ulendo Wobwereza Woyamba: (Osapitirira 3 min.) Gwiritsani ntchito chitsanzo cha ulendo wobwereza woyamba. (th phunziro 2)
Ulendo Wobwereza Woyamba: (Osapitirira 4 min.) Yambani ndi chitsanzo cha ulendo wobwereza woyamba. Musonyezeni buku la Zimene Baibulo Limaphunzitsa. (th phunziro 3)
MOYO WATHU WACHIKHRISTU
“Lamulo Lovomereza Ntchito Yathu Yolalikira ku Quebec”: (15 min.) Nkhani yokambirana. Onerani vidiyoyi.
Phunziro la Baibulo la Mpingo: (30 min.) jy mutu 22
Mfundo Zimene Taphunzira Komanso za Mlungu Wamawa (3 min.)
Nyimbo Na. 81 ndi Pemphero