Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • mwb20 November tsamba 2
  • Mose Anatsatira Malangizo Mosamala Kwambiri

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • Mose Anatsatira Malangizo Mosamala Kwambiri
  • Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—Ndandanda ya Misonkhano—2020
  • Nkhani Yofanana
  • Kodi Mumatsatira Malangizo?
    Nsanja ya Olonda​—1990
  • Kumvera Kumaposa Nsembe
    Kabuku ka Msonkhano wa Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—2022
  • Malangizo Okhudza Abale Amene Amakamba Nkhani pa Msonkhano wa Utumiki
    Utumiki Wathu wa Ufumu—2010
  • Phunzirani Njira za Yehova
    Nsanja ya Olonda—2005
Onani Zambiri
Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—Ndandanda ya Misonkhano—2020
mwb20 November tsamba 2

CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU | EKISODO 39-40

Mose Anatsatira Malangizo Mosamala Kwambiri

39:32, 43; 40:1, 2, 16

Mose anatsatira mosamala malangizo onse a Yehova okhudza kumanga komanso kuimika chihema. Ifenso tiyenera kumvetsera malangizo alionse amene tingalandire kuchokera ku gulu la Yehova n’kuwatsatira mwamsanga komanso ndi mtima wonse. Zimenezi n’zofunika ngakhale pamene tikuona kuti kuwatsatira si kofunika kapena sitikuwamvetsa.​—Lu 16:10.

N’chifukwa chiyani tiyenera kumvetsera komanso kutsatira mosamala malangizo amene talandira . . .

  • pamsonkhano wokonzekera utumiki?

  • okhudza kukonzekera matenda a mwadzidzidzi?

  • okhudza kukonzekera ngozi zadzidzidzi?

Abale ndi alongo akutsatira malangizo amene alandira. 1. Kagulu ka utumiki kakukonzekera utumiki pakhonde. 2. Mlongo akulemba zimene wasankha pa nkhani ya thandizo la kuchipatala pa khadi lake. 3. Banja likuika zinthu zofunika kutenga pakachitika ngozi zadzidzidzi mu kachikwama.
    Mabuku a Chichewa (1974-2025)
    Tulukani
    Lowani
    • Chichewa
    • Tumizirani Ena
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • Privacy Settings
    • JW.ORG
    • Lowani
    Tumizirani Ena