Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • mwb24 May tsamba 10-11
  • June 10-16

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • June 10-16
  • Utumiki Komanso Moyo Wathu wa Chikhristu—Kabuku ka Msonkhano—2024
Utumiki Komanso Moyo Wathu wa Chikhristu—Kabuku ka Msonkhano—2024
mwb24 May tsamba 10-11

JUNE 10-16

MASALIMO 48-50

Nyimbo Na. 126 ndi Pemphero | Mawu Oyamba (1 min.)

CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

1. Makolo, Muzithandiza Banja Lanu Kudalira Kwambiri Gulu la Yehova

(10 min.)

Muzithandiza ana anu kuti azikonda kwambiri Yehova komanso gulu lake (Sl 48:12, 13; w22.03 22 ¶11; w11 3/15 19 ¶5-7)

Muziphunzitsa ana anu mbiri ya gulu lathu (w12 8/15 12 ¶5)

Muzikhala chitsanzo pophunzitsa ana anu kutsatira malangizo ochokera ku gulu la Yehova (Sl 48:14)

Zithunzi: 1. Bambo akukambirana ndi mwana wake mfundo zina zopezeka m’buku la “Gulu Lochita Chifuniro cha Yehova.” 2. Banja likuonera pulogalamu ya JW Broadcasting. 3. Banja lina likuona malo osungirako zinthu zakale ku Beteli. 4. Mayi akugwiritsa ntchito “Buku Lapachaka la Mboni za Yehova” komanso buku la Chingelezi lakuti “Jehovah’s Witnesses​—Proclaimers of God’s Kingdom” pophunzira ndi mwana wake.

ZOMWE MUNGACHITE PA KULAMBIRA KWA PABANJA: Nthawi ndi nthawi muzionera ndi kukambirana mavidiyo opezeka pa gawo lakuti “Gulu Lathu” pa jw.org.

2. Mfundo Zothandiza

(10 min.)

  • Sl 49:6, 7​—Kodi Aisiraeli ankafunika kumakumbukira chiyani zokhudza chuma chimene anali nacho? (it-2 805)

  • Kodi ndi mfundo ziti zimene mwapeza pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno?

3. Kuwerenga Baibulo

(4 min.) Sl 50:1-23 (th phunziro 11)

KUPHUNZITSA MWALUSO MU UTUMIKI

4. Kulimba Mtima​—Zomwe Yesu Anachita

(7 min.) Nkhani yokambirana. Onerani VIDIYO, kenako kambiranani kabuku ka lmd phunziro 6 mfundo 1-2.

5. Kulimba Mtima​—Zomwe Mungachite Potsanzira Yesu

(8 min.) Nkhani yokambirana kuchokera mu kabuku ka lmd phunziro 6 mfundo 3-5 ndi “Onaninso Malemba Awa.”

MOYO WATHU WA CHIKHRISTU

Nyimbo Na. 73

6. Zofunika Pampingo

(15 min.)

7. Phunziro la Baibulo la Mpingo

(30 min.) bt mutu 11 ¶1-4, mawu ofotokoza gawo 4 ndi bokosi patsamba 86-87

Mawu Omaliza (3 min.) | Nyimbo Na. 103 ndi Pemphero

    Mabuku a Chichewa (1974-2025)
    Tulukani
    Lowani
    • Chichewa
    • Tumizirani Ena
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • Privacy Settings
    • JW.ORG
    • Lowani
    Tumizirani Ena