FEBRUARY 2-8
YESAYA 30-32
Nyimbo Na. 8 ndi Pemphero | Mawu Oyamba (1 min.)
1. Pezani Chitetezo M’mapiko a Yehova
(10 min.)
Yehova amateteza anthu ake ngati mmene mbalame imatetezera ana ake (Yes 31:5; w01 11/15 16 ¶7-mwbr)
Pitirizani kudalira anthu amene Yehova amawagwiritsa ntchito kuti akuthandizeni (Yes 32:1, 2; w24.01 24 ¶13-mwbr)
Chiyembekezo chimene Yehova wapereka chingakupatseni mphamvu (Yes 32:16-18; w23.10 17 ¶19-mwbr)
2. Mfundo Zothandiza
(10 min.)
Yes 30:20—Kodi mawu akuti “mavuto kuti akhale chakudya chanu ndi kuponderezedwa kuti kukhale madzi anu” akutanthauza chiyani? (it-E “Chakudya” ¶6-mwbr)
Kodi ndi mfundo ziti zimene mwapeza pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno?
3. Kuwerenga Baibulo
(4 min.) Yes 31:1-9 (th phunziro 10)
4. Ulendo Woyamba
(4 min.) KULALIKIRA MWAMWAYI. Munthuyo akufotokoza kuti akuda nkhawa ndi zinthu zimene zangochitika kumene. (lmd phunziro 2, mfundo 5)
5. Ulendo Woyamba
(4 min.) KUNYUMBA NDI NYUMBA. (lmd phunziro 5, mfundo 5)
6. Ulendo Wobwereza
(4 min.) KUNYUMBA NDI NYUMBA. M’pempheni kuti muziphunzira naye Baibulo. (lmd phunziro 7, mfundo 3)
Nyimbo Na. 157
7. “Ntchito ya Chilungamo Chenicheni Idzakhala Mtendere”—Kachigawo Kake
(15 min.) Nkhani yokambirana.
Onerani VIDIYO. Kenako funsani funso ili:
Kodi mwaphunzira chiyani zokhudza chilungamo chenicheni muvidiyoyi?—Yes 32:17.
8. Phunziro la Baibulo la Mpingo
(30 min.) lfb mutu 58-59