FEBRUARY 9-15
YESAYA 33-35
Nyimbo Na. 3 ndi Pemphero | Mawu Oyamba (1 min.)
1. “Mʼmasiku Anu, Iye Adzachititsa Kuti Muzimva Kuti Ndinu Otetezeka”
(10 min.)
Muzipempha Yehova kuti akulimbitseni mukamayesedwa (Yes 33:6a; w24.01 22 ¶7-8-mwbr)
Muzimupempha kuti akupatseni nzeru kuti muzisankha bwino zinthu (Yes 33:6b; w21.02 29 ¶10-11-mwbr)
Mukamadalira Yehova mungaone kukwaniritsidwa kwa lemba la Yesaya 33:24 (ip-1 352-355 ¶21-22-mwbr)
Kugwiritsa ntchito zinthu zofufuzira kungakuthandizeni kukhala olimba
2. Mfundo Zothandiza
(10 min.)
Yes 35:8—Kodi “Msewu Wopatulika” umaimira chiyani masiku ano? (w23.05 15 ¶8-mwbr)
Kodi ndi mfundo ziti zimene mwapeza pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno?
3. Kuwerenga Baibulo
(4 min.) Yes 35:1-10 (th phunziro 12)
4. Ulendo Woyamba
(3 min.) KULALIKIRA M’MALO OPEZEKA ANTHU AMBIRI. Muitanireni ku misonkhano yathu. (lmd phunziro 3, mfundo 3)
5. Ulendo Wobwereza
(4 min.) KUNYUMBA NDI NYUMBA. Gwiritsani ntchito vidiyo ya pagawo la Zinthu Zophunzitsira (Teaching Toolbox) pa JW Library. (lmd phunziro 9, mfundo 5)
6. Nkhani
(5 min.) lmd zakumapeto A, mfundo 15—Mutu: Baibulo Limatiphunzitsa Mmene Tingapempherere. (th phunziro 14)
Nyimbo Na. 41
7. Zofunika Pampingo
(15 min.)
8. Phunziro la Baibulo la Mpingo
(30 min.) lfb mutu 60-61