FEBRUARY 16-22
YESAYA 36-37
Nyimbo Na. 150 ndi Pemphero | Mawu Oyamba (1 min.)
1. “Usachite Mantha Chifukwa cha Mawu Amene Wamva”
(10 min.)
Rabisake anapita ku Yerusalemu kukaopseza anthu a Yehova (Yes 36:1, 2; it-E “Hezekiya” Na. 1 ¶14-mwbr)
Iye ankafuna kuti anthuwo azidziona kuti alibe mphamvu komanso wowathandiza (Yes 36:8; ip-1 387 ¶10-mwbr)
Iye anawanyoza chifukwa chodalira Yehova ndi anthu amene ankawatsogolera (Yes 36:7, 18-20; ip-1 388 ¶13-14-mwbr)
Anthu a Yehova sayenera kuchita mantha ndi anthu amene amawavutitsa.—Yes 37:6, 7
ZIMENE MUNGACHITE PA KULAMBIRA KWA PABANJA: Onerani VIDIYO yakuti “Inu Yehova, . . . Chikhulupiriro Changa Chili Mwa Inu,” kenako mukambirane zimene mwaphunzira.
2. Mfundo Zothandiza
(10 min.)
Yes 37:29—Kodi Yehova anamanga zingwe pakamwa pa Senakeribu m’njira yotani? (it-E “Zingwe” ¶4-mwbr)
Kodi ndi mfundo ziti zimene mwapeza pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno?
3. Kuwerenga Baibulo
(4 min.) Yes 37:14-23 (th phunziro 2)
4. Ulendo Woyamba
(3 min.) KUNYUMBA NDI NYUMBA. Kambiranani mfundo imodzi ya choonadi mu zakumapeto A, m’kabuku kakuti Muzikonda Anthu. (lmd phunziro 1, mfundo 4)
5. Ulendo Woyamba
(4 min.) KULALIKIRA MWAMWAYI. (lmd phunziro 3, mfundo 5)
6. Kufotokoza Zimene Mumakhulupirira
(5 min.) Chitsanzo. ijwbq Na. 110 ¶1-4-mwbr—Mutu: Kodi Ubatizo Umatanthauza Chiyani? (th phunziro 17)
Nyimbo Na. 118
7. “Kodi Ukudalira Chiyani?”
(15 min.) Nkhani yokambirana.
Kodi munthu wina anakutsutsanipo kapena kukunyozani chifukwa chokhulupirira Mulungu, Baibulo kapenanso chifukwa chosankha kukhala wa Mboni za Yehova? N’kutheka kuti munachita mantha. Zimene ena amalankhula zingachititsenso kuti muzikayikira zimene mumakhulupirira. Kodi mungatani kuti musachite mantha kapena kukayikira?
Werengani Yesaya 36:4. Kenako funsani funso ili:
N’chifukwa chiyani n’zofunika kukhala ndi zifukwa zamphamvu pa zimene timakhulupirira?
Onerani VIDIYO yakuti Moyo Wanga Wachinyamata—Kodi N’zomveka Kukhulupirira Kuti Mulungu Alipo? Kenako funsani mafunso awa:
Kodi Elibaldo ndi Crystal anatani kuti azikhulupirira kwambiri zimene Baibulo limaphunzitsa?
N’chiyani chimakutsimikizirani inuyo kuti Mulungu alipo?
Kodi ndi malemba ati amene amakutsimikizirani kuti . . .
Yehova amakukondani?
nthawi zonse Yehova adzakuthandizani?
munapezadi anthu a Mulungu?
8. Phunziro la Baibulo la Mpingo
(30 min.) lfb mutu 62-63