MARCH 9-15
YESAYA 43-44
Nyimbo Na. 63 ndi Pemphero | Mawu Oyamba (1 min.)
1. Ulosi Umene Unalembedwa Kutatsala Zaka 200
(10 min.)
Mitsinje ya Babulo ‘idzaumitsidwa’ (Yes 44:27; gm 123-124 ¶16-17-mwbr)
Koresi adzakhala ngati “m’busa” wa Mulungu pogonjetsa Babulo (Yes 44:28a; it-E “Koresi” ¶7-mwbr)
Koresi adzatumiza anthu a Mulungu kuti akamangenso mzinda komanso kachisi (Eza 1:1-3; Yes 44:28b; it-E “Koresi” ¶17-mwbr)
FUFUZANI: Kodi Koresi anakwaniritsa bwanji ulosi wa pa Yesaya 45:1-4?
2. Mfundo Zothandiza
(10 min.)
Yes 44:28—Kodi tikudziwa bwanji kuti Yehova sanakakamize Koresi kuti azimulambira? (w24.02 30 ¶8-mwbr)
Kodi ndi mfundo ziti zimene mwapeza pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno?
3. Kuwerenga Baibulo
(4 min.) Yes 44:9-20 (th phunziro 10)
4. Ulendo Woyamba
(1 min.) KUNYUMBA NDI NYUMBA. Mugawireni kapepala koitanira anthu ku Chikumbutso. (lmd phunziro 4, mfundo 3)
5. Ulendo Woyamba
(3 min.) KULALIKIRA MWAMWAYI. Itanirani mnzanu kumwambo wa Chikumbutso. (lmd phunziro 3, mfundo 4)
6. Ulendo Woyamba
(3 min.) KULALIKIRA MWAMWAYI. Pemphani abwana anu kuti patsiku la Chikumbutso adzakuloleni kuti musadzagwire ntchito. (lmd phunziro 6, mfundo 3)
7. Ulendo Wobwereza
(4 min.) KUNYUMBA NDI NYUMBA. Pemphani munthu amene pa ulendo wapita analandira kapepala koitanira anthu ku Chikumbutso kuti muziphunzira naye Baibulo. (lmd phunziro 7, mfundo 4)
Nyimbo Na. 69
8. Zofunika Pampingo
(15 min.)
9. Phunziro la Baibulo la Mpingo
(30 min.) ) lfb mawu oyamba a gawo 11 ndi mutu 68-69