Zamkatimu
Kalata Yochokera ku Bungwe Lolamulira 4
Zimene zachitika m’chaka chapitachi 8
“Timakonda Kwambiri TV ya JW Broadcasting” 10
Pakufunika Kumanga Nyumba za Ufumu Mofulumira 16
Kodi Ntchito Yomanga Ikuyenda Bwanji ku Warwick? 18
Njira Imene Ikuthandiza Kulalikira Anthu Omwe Sapezeka Pakhomo 20
Mwambo Wotsegulira Maofesi a Nthambi 28
Baibulo la Dziko Lapansi Latsopano Lamasuliridwa M’zinenero Zinanso Zambiri 30
Malipoti Apadera Zochitika M’mayiko Osiyanasiyana 39
Ntchito Yolalikira ndi Kuphunzitsa Padziko Lonse 44
Mfundo Zachidule Zokhudza Dziko la Indonesia 82
Malonda a Zokometsera Chakudya 86
“Ndikufuna Kukayambira Apa” 88
Njira Zimene Poyamba Ankagwiritsa Ntchito Polalikira 97
Kunayambika Kagulu Kenakake ka Chipembedzo 100
Ankaona Kuti Kukhala pa Ubwenzi ndi Yehova N’kofunika Kwambiri 101
Ntchito Yolalikira Inabala Zipatso ku West Java 102
Ulamuliro Wankhanza wa Boma la Japan 108
Amishonale Anayamba Kufika ku Indonesia 114
Ntchito Yolalikira Inafika Mpaka ku Zilumba Zakum’mawa 119
Ankachita Zinthu Ngati Sara Weniweni 126
Ndinapulumuka Pamene Chipani cha Chikomyunizimu Chinkafuna Kulanda Boma 129
Anachita Upainiya Wapadera kwa Zaka 50 130
Poyamba Anali Mtsogoleri wa Zigawenga Koma Kenako Anakhala Nzika Yabwino 131
Anatsimikiza Mtima Kuti Sabwerera M’mbuyo 132
Amakondana Ngakhale pa Nthawi ya Mavuto 143
Sitinalole Kusiya Zimene Timakhulupirira 144
Tinapulumuka Chifukwa Chotsatira Malangizo 145
Ntchito Yathu Inayambanso Kuyenda Bwino 146
Abale Ankalengeza za Yehova Molimba Mtima 151
Ofesi ya Nthambi Yomwe Ili M’mwamba Kwambiri 158
Yehova Anatichitira Zinthu Zoposa Zimene Tinkayembekezera 168
Tinasangalala Titadziwa Kuti Ndife Pachibale 170
Zimene Zinachitika Zaka 100 Zapitazo mu 1916 172
Mwambo Wokumbukira Imfa ya Yesu Lachisanu pa 3 April, 2015 177