Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • nwt tsamba 2236-2237
  • B12-B Wiki Yomaliza ya Moyo wa Yesu Padziko Lapansi (Gawo 2)

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • B12-B Wiki Yomaliza ya Moyo wa Yesu Padziko Lapansi (Gawo 2)
  • Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
  • Timitu
  • Nkhani Yofanana
  • Yerusalemu ndi Madera Ozungulira
  • Nisani 12
  • Nisani 13
  • Nisani 14
  • Nisani 15 (Sabata)
  • Nisani 16
  • B12-A Wiki Yomaliza ya Moyo wa Yesu Padziko Lapansi (Gawo 1)
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
  • Ndandanda Yowerengera Baibulo pa Nyengo ya Chikumbutso cha 2023
    Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—2023
  • Ndandanda Yowerengera Baibulo pa Nyengo ya Chikumbutso cha 2022
    Kabuku ka Msonkhano wa Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—2022
  • Ndandanda Yowerengera Baibulo pa Nyengo ya Chikumbutso cha 2024
    Utumiki Komanso Moyo Wathu wa Chikhristu—Kabuku ka Msonkhano—2024
Onani Zambiri
Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
B12-B Wiki Yomaliza ya Moyo wa Yesu Padziko Lapansi (Gawo 2)

B12-B

Wiki Yomaliza ya Moyo wa Yesu Padziko Lapansi (Gawo 2)

Losindikizidwa
Tchati chosonyeza zimene zinachitika mu 33 C.E., chaka chimene Yesu anaphedwa.

Yerusalemu ndi Madera Ozungulira

Mapu a Yerusalemu ndi madera ozungulira. Mapuwa akusonyeza madera odziwika komanso amene akuwaganizira. 1. Kachisi. 2. Munda wa Getsemane. 3. Nyumba ya Bwanamkubwa. 4. Nyumba ya Kayafa. 5. Nyumba imene Herode Antipa ankakhala. 6. Damu la Betizata. 7. Dziwe la Siloamu. 8. Holo ya Khoti Lalikulu la Ayuda. 9. Gologota. 10. Munda Wamagazi.
  1. Kachisi

  2. Munda wa Getsemane (?)

  3. Nyumba ya Bwanamkubwa

  4. Nyumba ya Kayafa (?)

  5. Nyumba imene Herode Antipa ankakhala (?)

  6. Damu la Betizata

  7. Dziwe la Siloamu

  8. Holo ya Khoti Lalikulu la Ayuda (?)

  9. Gologota (?)

  10. Munda Wamagazi (?)

Sankhani tsiku: Nisan 12 | Nisan 13 | Nisan 14 | Nisan 15 | Nisan 16

Nisani 12

MADZULO (Masiku a Ayuda amayamba ndi kutha dzuwa litalowa)

M’MAWA

  • Yuda Isikariyoti ndi atsogoleri achipembedzo cha Chiyuda akukonza chiwembu.

    Yesu ndi ophunzira ake

  • Yudasi anakonza zoti apereke Yesu

  • Mateyu 26:1-5, 14-16

  • Maliko 14:1, 2, 10, 11

  • Luka 22:1-6

MADZULO

Bwererani koyambirira

Nisani 13

MADZULO

M’MAWA

  • Petulo ndi Yohane akutsatira munthu amene wasenza mtsuko wamadzi.

    Petulo ndi Yohane akukonzekera Pasika

  • Yesu ndi atumwi ake ena anafika madzulo

  • Mateyu 26:17-19

  • Maliko 14:12-16

  • Luka 22:7-13

MADZULO

Bwererani koyambirira

Nisani 14

MADZULO

  • Yesu ndi atumwi ake okhulupirika akhala patebulo pa nthawi ya Chakudya Chamadzulo cha Ambuye.

    Anadya Pasika ndi atumwi ake

  • Anasambitsa mapazi a atumwi ake

  • Anauza Yudasi kuti achoke

  • Anayambitsa mwambo wa Chakudya Chamadzulo cha Ambuye

  • Mateyu 26:20-35

  • Maliko 14:17-31

  • Luka 22:14-38

  • Yohane 13:1–17:26

  • Yesu ali pakhonde ndipo akuyang’ana Petulo amene akumukana pamaso pa anthu amene asonkhana m’bwaloli.

    Anaperekedwa n’kumangidwa m’munda wa Getsemane (2)

  • Atumwi anathawa

  • Anaimbidwa mlandu ndi Khoti Lalikulu la Ayuda (4)

  • Petulo anakana Yesu

  • Mateyu 26:36-75

  • Maliko 14:32-72

  • Luka 22:39-65

  • Yohane 18:1-27

M’MAWA

  • Yesu wavala chisoti chaminga komanso chinsalu chapepo ndipo Pilato akumupereka kwa anthu okwiya.

    Anakaonekeranso m’Khoti Lalikulu la Ayuda (8)

  • Anapita naye kwa Pilato (3), kenako kwa Herode (5), n’kubwereranso kwa Pilato (3)

  • Nikodemo, Yosefe wa ku Arimateya ndi ophunzira ena akukonza mtembo wa Yesu pokonzekera kuti amuike m’manda.

    Anaweruzidwa kuti aphedwe ndipo anaphedwera ku Gologota (9)

  • Anafa cha m’ma 3 koloko madzulo

  • Anachotsa mtembo wake n’kukauika m’manda

  • Mateyu 27:1-61

  • Maliko 15:1-47

  • Luka 22:66–23:56

  • Yohane 18:28–19:42

MADZULO

Bwererani koyambirira

Nisani 15 (Sabata)

MADZULO

M’MAWA

  • Pilato anavomereza zoika alonda pamanda a Yesu

  • Mateyu 27:62-66

MADZULO

Bwererani koyambirira

Nisani 16

MADZULO

  • Anagula zonunkhiritsa zina zopaka mtembo wa Yesu

  • Maliko 16:1

M’MAWA

  • Mariya wa ku Magadala akusuzumira m’manda a Yesu opanda kanthu.

    Anaukitsidwa

  • Anaonekera kwa ophunzira ake

  • Mateyu 28:1-15

  • Maliko 16:2-8

  • Luka 24:1-49

  • Yohane 20:1-25

MADZULO

Bwererani koyambirira

    Mabuku a Chichewa (1974-2025)
    Tulukani
    Lowani
    • Chichewa
    • Tumizirani Ena
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • Privacy Settings
    • JW.ORG
    • Lowani
    Tumizirani Ena