Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • nwt tsamba 2051
  • Zimene Zili Mʼbuku la 1 Petulo

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • Zimene Zili Mʼbuku la 1 Petulo
  • Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
  • Nkhani Yofanana
  • Zimene Zili Mʼbuku la Aroma
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
  • Zimene Zili mu 2 Yohane
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
  • Akazi, Muzilemekeza Kwambiri Amuna Anu
    Nsanja ya Olonda—2007
  • Tayani Nkhaŵa Yanu Yonse pa Yehova
    Nsanja ya Olonda—1994
Onani Zambiri
Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
Zimene Zili Mʼbuku la 1 Petulo

1 PETULO

ZIMENE ZILI MʼBUKULI

  • 1

    • Moni (1, 2)

    • Kubadwanso mwatsopano nʼkukhala ndi chiyembekezo chodalirika (3-12)

    • Mukhale oyera monga ana omvera (13-25)

  • 2

    • Muzilakalaka Mawu a Mulungu (1-3)

    • Miyala yamoyo ikumangidwa nʼkukhala nyumba yauzimu (4-10)

    • Muzikhala ngati alendo mʼdzikoli (11, 12)

    • Muzigonjera anthu oyenera kuwagonjera (13-25)

      • Khristu ndi chitsanzo chathu (21)

  • 3

    • Akazi komanso amuna apabanja (1-7)

    • Muzimverana chisoni; muziyesetsa kumakhala mwamtendere (8-12)

    • Kuvutika chifukwa chochita zinthu mwachilungamo (13-22)

      • Muzikhala okonzeka kufotokoza za chiyembekezo chanu (15)

      • Ubatizo komanso chikumbumtima chabwino (21)

  • 4

    • Muzichita zimene Mulungu amafuna, ngati mmene Khristu ankachitira (1-6)

    • Mapeto a zinthu zonse ayandikira (7-11)

    • Kuvutika chifukwa chokhala Mkhristu (12-19)

  • 5

    • Wetani gulu la nkhosa za Mulungu (1-4)

    • Mukhale odzichepetsa komanso atcheru (5-11)

      • Muzitula nkhawa zanu zonse kwa Mulungu (7)

      • Mdyerekezi ali ngati mkango wobangula (8)

    • Mawu omaliza (12-14)

    Mabuku a Chichewa (1974-2025)
    Tulukani
    Lowani
    • Chichewa
    • Tumizirani Ena
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • Privacy Settings
    • JW.ORG
    • Lowani
    Tumizirani Ena