Zamkatimu
July 8, 2000
Kodi Moyo N’ngwotsika Mtengo Chonchi?
M’zaka zaposachedwapa kukukhala ngati kwayambika “chikhalidwe cha imfa” pakati pa achinyamata. Kodi chikuchititsa khalidweli n’chiyani? Kodi pali njira yolithetsera?
3 Kodi Moyo Ukutsikiratsikira Mtengo?
5 Kodi “Chikhalidwe cha Imfa” Chimalimbikitsidwa Motani?
8 Kuthandiza Achinyamata Kuthawa “Chikhalidwe cha Imfa”
11 Nkhani Zokopa Zingaphetse Anthu
17 Musanyengedwe ndi Nkhani Zokopa!
20 Kodi Ndizimwa Asipilini Tsiku N’tsiku?
32 “Ndimakonda Mmene Imalongosolera Nkhani”
Kwa anthu amene amakwera matola, kodi ndi machenjezo ati amene ali ofunika kuti asagwe m’mavuto?
Mwetulirani—N’zothandiza kwa Inu! 29
Kodi kumwetulira kungakuthandizeni m’njira iliyonse m’moyo wanu wa tsiku n’tsiku?
[Mawu a Chithunzi patsamba 2]
AP Photo/Laura Rauch