Zamkatimu
February 8, 2002
Kodi Othaŵa Nkhondo Adzapezadi Malo Okhazikika?
Padziko lonse, anthu othaŵa kwawo amangoyendayenda atasoŵa pogwira. Anthu ambiri pa gululi sapeza n’komwe bata limene amafunafunalo. Kodi ilipo nthaŵi ina imene aliyense adzakhaleko ndi malo omati ndiye kwawo?
3 Anthu Amene Akufunafuna Bata
6 Kupeza Malo Amene Angamati Ndiye Kwawo
11 Dziko Limene Aliyense Angaloledwe Kudzakhalamo
14 Mbidzi—Hatchi ya mu Africa Yongodziyendera Mmene Ikufunira
21 “Tsiku Losangalatsa Kwambiri M’moyo Wathu”
22 Tsiku Laukwati N’losangalatsa Komanso N’losautsa
27 Ukwati Uyenera Kukhala Mgwirizano Wosatha
32 “Chonde Ndithandizeni! Ndinu Nokha Amene Ndikudalira”
Kodi Pali Vuto Ngati Nditachitako Chidwi Pang’ono Ndi Zamatsenga? 18
Achinyamata ambiri amachita chidwi ndi zamatsenga. Kodi n’zosangalatsadi kapena zikhoza kum’vulaza munthu?
Kodi Mikaeli Mngelo Wamkulu Ndani? 30
M’Baibulo angelo aŵiri okha ndi amene anawatchula mayina awo. Tiyeni tim’dziŵe mngelo weniweni wotchedwa Mikaeli.
[Chithunzi pachikuto]
Pa chikuto: Othaŵa nkhondo a ku Rwanda akubwerera kwawo
[Mawu a Chithunzi]
UNHCR/R. Chalasani
[Chithunzi pamasamba 2, 3]
Pa masamba 2 ndi 3: Othaŵa kwawo a ku Ethiopia akudikirira kulandira chakudya ndi madzi
[Mawu a Chithunzi]
UN PHOTO 164673/JOHN ISAAC