Zamkatimu
May 2007
Kulimbana ndi Umphawi M’dziko Lokondera
Masiku ano, mayiko ambiri n’ngolemera komano anthu ambirimbiri ali paumphawi wadzaoneni. Kodi anthu osauka angayembekezere kusintha kulikonse?
3 Kodi Ndani Akudyerera Chuma cha Dzikoli?
4 N’chifukwa Chiyani Ambiri Ali Osauka M’dziko Lolemerali?
7 Kodi Osauka Angayembekezere Zotani?
14 Adziweni Anthu a ku East Timor
23 “Mbalame ya Chinsansa” mu ngalande za ku Venice
28 N’chifukwa Chiyani Muyenera Kumakaonana ndi Dokotala wa Mano?
32 Kodi Ndani Ali Otsatira Oona a Khristu?
Kodi Mulungu Analemberatu Tsogolo Lanu? 12
Kodi Mulungu anakonzeratu kapena kulemberatu mapeto a zochita zanu zonse ndiponso nthawi yeniyeni imene mudzafe?
Kodi Munthu Ameneyu Ndi Woyenera Kumanga Naye Banja? 18
Kodi mungadziwe bwanji kuti munthu amene muli naye pachibwenzi n’ngoyenerera kumanga naye banja?