Zamkatimu
August 2010
Kodi Mumadziwa Zotani Zokhudza Mboni za Yehova?
Kodi mwamvapo zotani zokhudza Mboni za Yehova? Kodi zimene munamvazo n’zoona? Tikukhulupirira kuti nkhanizi zikuthandizani kudziwa zoona zenizeni.
3 Kodi Mumadziwa Zotani Zokhudza Mboni za Yehova?
6 Mafunso Amene Anthu Amakonda Kufunsa
8 Kodi Mboni za Yehova Zimakhulupirira Chiyani?
10 Loya Amene Anafufuza Zimene Mboni za Yehova Zimaphunzitsa
22 Ndikungoona Kuchedwa Kuti Ndidzawauze Kuti, “Tonse Tilipo”
24 Mahatchi Ofatsa Koma Amphamvu
32 Kodi Mboni za Yehova Zimaphunzitsa Bwanji Baibulo?
Matenda Otupa Chiwindi Amapha Mwakabisira 12
Pafupifupi munthu mmodzi pa anthu atatu alionse padziko lonse ali ndi matenda amenewa. Matendawa ndi oopsa kwambiri ndipo amapha. Werengani nkhaniyi kuti mudziwe mmene mungadzitetezere.
Kodi Mumawadziwa Anthu Otchedwa a Batak? 16
Ku Indonesia kuli anthu ambiri a mtundu wa Batak ndipo chiwerengero chawo chimaposa mitundu ina yonse ya m’dzikoli. Dera limene anthuwa amakhala ndi lokongola kwambiri ndipo nyengo yake ndi yabwino. Werengani nkhaniyi kuti muphunzire zambiri zokhudza chikhalidwe cha anthu amenewa.
[Mawu a Chithunzi patsamba 2]
© Sebastian Kaulitzki/Alamy