Zamkatimu
January 2013
© 2013 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania. Ulamuliro wonse pa magazini ino n’ngwathu.
NKHANI ZOYAMBILIRA: Mmene Mungalerere Ana Anu Kuti Asakhale Odzikonda Tsamba 8 Mpaka 11
MUNGAPEZE ZAMBIRI PA WEBUSAITI YA
ACHINYAMATA
ZIMENE ACHINYAMATA AMADZIFUNSA
Kodi Ndizitani Ngati Ena Akundichitira Zachipongwe?
Mtsikana wina, dzina lake Coretta ananena kuti: “Ku sukulu kwathu, anyamata ankandikoka khamisolo, n’kumandiuza zinthu zopusa ngati mmene ndingasangalalire nditati ndagona nawo.” Kodi mukanakhala inuyo mukanatani? Anthu akhoza kusiya kukuchitirani zachipongwe ngati mutadziwa zoyenera kuchita ngati anthu akukuchitirani zachipongwe.
ANA
ZITHUNZI
Chitani dawunilodi ndi kupulinta chithunzi. Kenako malizitsani chithunzicho limodzi ndi ana anu. Athandizeni kudziwa zambiri za anthu a m’Baibulo komanso kuphunzira makhalidwe abwino.