Zamkatimu
March 2013
© 2013 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania. Ulamuliro wonse pa magazini ino n’ngwathu.
NKHANI YA PACHIKUTO: Kodi Bambo Wabwino Amatani? 4-7
MUNGAPEZE ZAMBIRI PA WEBUSAITI YA
ACHINYAMATA
ZIMENE ACHINYAMATA AMADZIFUNSA
Kodi Ndingatani Kuti Ndisamazengereze Pochita Zinthu?
Kodi nthawi zambiri mumachedwa kumaliza ntchito zapakhomo kapena kulemba homuweki? N’kutheka kuti mumachedwa chifukwa mumazengereza pochita zinthu ndipo muyenera kusintha. Nkhaniyi ikuthandizani kupewa kuzengereza kugwira ntchito chifukwa choona kuti simungaikwanitse, simuikonda kapena ngati muli ndi zochita zambiri.
(Fufuzani pa mawu akuti ZIMENE BAIBULO LIMAPHUNZITSA/ACHINYAMATA)
ANA
Werengani nkhani zomwe zafotokozedwa pogwiritsa ntchito zithunzi. Gwiritsani ntchito nkhanizi kuthandizira ana anu kudziwa zambiri za anthu otchulidwa m’Baibulo komanso kuwathandiza kuti akhale ndi makhalidwe abwino.
(Fufuzani pa mawu akuti ZIMENE BAIBULO LIMAPHUNZITSA/ANA)