Zamkatimu
January 2013
© 2013 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania. Ulamuliro wonse pa magazini ino n’ngwathu.
NKHANI YA PACHIKUTO: KODI OSAMUKIRA KUDZIKO LINA AMAKAPEZADI ZIMENE AKUFUNA? Tsamba 6 Mpaka 9
MUNGAPEZE ZAMBIRI PA WEBUSAITI YA
ACHINYAMATA
ZIMENE ACHINYAMATA AMADZIFUNSA
Kodi Ndiyenera Kudziwa Zotani Zokhudza Mameseji a Pafoni?
Mameseji amathandiza kwambiri kuti anthu azilankhulana. Koma ngati agwiritsidwa ntchito molakwika, akhoza kuwononga mbiri yanu komanso kuchititsa kuti anthu asamacheze nanu. Pezani malangizo okhudza anthu amene muyenera kumalemberana nawo mameseji, nkhani zake komanso nthawi yoyenera kulemberana mamesejiwo.
(Fufuzani pa mutu wakuti ZIMENE BAIBULO LIMAPHUNZITSA/ACHINYAMATA)
ANA
Werengani limodzi ndi ana anu nkhani za m’Baibulo zofotokozedwa pogwiritsa ntchito zithunzi. Kenako gwiritsani ntchito masamba omwe ali ndi zoti muchite ndi ana powathandiza kudziwa za anthu ofotokozedwa m’Baibulo komanso makhalidwe abwino.
(Fufuzani pa mutu wakuti ZIMENE BAIBULO LIMAPHUNZITSA/ANA)