Zamkatimu
May 2013
© 2013 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania. Ulamuliro wonse pa magazini ino n’ngwathu.
NKHANI YA PACHIKUTO: Chenjerani ndi Mbava Komanso Anthu Ogwiririra Tsamba 6 mpaka 9
MUNGAPEZE ZAMBIRI PA WEBUSAITI YA
ACHINYAMATA
ZIMENE ACHINYAMATA AMADZIFUNSA
Kodi Ndingatani ngati Ndikudwala Matenda Aakulu? (Gawo 1)
Mtsikana wina, dzina lake Yeimy, ananena kuti: “Kuyambira ndili mwana ndinkadwaladwala moti pamene ndinkakwanitsa zaka 11, ndinayamba kuyenda pa njinga ya olumala. Panopa sinditha kuchita zinthu zina ngakhale kunyamula zinthu zopepuka.” Werengani nkhaniyi kuti mudziwe zimene Yeimy komanso achinyamata ena atatu, omwe akudwala matenda aakulu, amachita kuti apilire matendawo.
(Fufuzani pa mawu akuti ZIMENE BAIBULO LIMAPHUNZITSA/ACHINYAMATA)
ANA
Werengani nkhani zomwe zafotokozedwa pogwiritsa ntchito zithunzi. Gwiritsani ntchito nkhanizi kuthandizira ana anu kudziwa zambiri za anthu otchulidwa m’Baibulo komanso kuwathandiza kuti akhale ndi makhalidwe abwino.
(Fufuzani pa mawu akuti ZIMENE BAIBULO LIMAPHUNZITSA/ANA)