Zamkatimu
June 2013
© 2013 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania. Ulamuliro wonse pa magazini ino n’ngwathu.
NKHANI YA PACHIKUTO: KODI N’KULAKWA KUGULA KATUNDU WAMBIRIMBIRI? TSAMBA 8-11
MUNGAPEZE ZAMBIRI PA WEBUSAITI YA
ACHINYAMATA
ZIMENE ACHINYAMATA AMADZIFUNSA
Kodi Ndimada Nkhawa Kwambiri Ndi Mmene Ndimaonekera?
Mtsikana wina wa zaka 15, dzina lake Serena, ananena kuti: “Nthawi zonse ndikadziyang’ana pagalasi ndimangodziona ngati ndine chimunthu chonyansa komanso chonenepa kwambiri. Moti nthawi ina ndinasiya kudya kuti ndionde.” Kodi mungatani ngati simusangalala ndi mmene mumaonekera?
(Fufuzani pa mawu akuti ZIMENE BAIBULO LIMAPHUNZITSA > ACHINYAMATA)
ANA
Werengani nkhani zomwe zafotokozedwa pogwiritsa ntchito zithunzi. Gwiritsani ntchito nkhanizi kuthandizira ana anu kudziwa zambiri za anthu otchulidwa m’Baibulo komanso kuwathandiza kuti akhale ndi makhalidwe abwino.
(Fufuzani pa mawu akuti ZIMENE BAIBULO LIMAPHUNZITSA > ANA)