Kodi Mungakonde Kumvetsa Zimene Baibulo Limaphunzitsa?
Simufunika
Kukhala wophunzira kwambiri
Kukhala ndi ndalama
Kumangokhulupirira zilizonse
Mukufunika
Kukhala ndi “luntha la kuganiza.”—Aroma 12:1
Kukhala wodzichepetsa
Zimene Baibulo limaphunzitsa zingakudabwitseni.