Musaleke Kuchita Zabwino
M’MAWA
9:30 Kumvetsera Nyimbo
9:40 Nyimbo Na. 77 ndi Pemphero
9:50 N’chifukwa Chiyani Timavutika Kuchita Zabwino?
10:05 Nkhani Yosiyirana: Muzipewa Kufesa Zopindulitsa Thupi
Muzigwiritsa Ntchito Malo Ochezera a pa Intaneti Moyenera
Muzisankha Zosangalatsa Zabwino
Muzipewa Mtima Wansanje
Konzani Tsogolo Labwino
11:05 Nyimbo Na. 45 ndi Zilengezo
11:15 Pitirizani Kuchitira Onse Zabwino
11:30 Kudzipereka Ndiponso Kubatizidwa
12:00 Nyimbo Na. 63
MASANA
1:10 Kumvetsera Nyimbo
1:20 Nyimbo Na. 127 ndi Pemphero
1:30 Nkhani ya Onse:Kodi Mungapewe Bwanji Kupusitsa Mulungu?
2:00 Phunziro Lachidule la Nsanja ya Olonda
2:30 Nyimbo Na. 59 ndi Zilengezo
2:40 Nkhani Yosiyirana: Pitirizani Kufesa Motsatira Mzimu wa Mulungu
Khalani ndi Chizolowezi Chophunzira
Muzigwiritsa Ntchito Mfundo za M’Baibulo Posankha Zochita
‘Dzanja Lanu Lisapume’
3:40 Tidzakolola Zabwino Tikapanda Kutopa
4:15 Nyimbo Na. 126 ndi Pemphero