‘Yembekezerani Yehova’
M’mawa
9:30 Kumvetsera Nyimbo
9:40 Nyimbo Na. 88 ndi Pemphero
9:50 Kodi Tingatani Kuti ‘Tiziyembekezera Yehova’ Mofunitsitsa?
10:05 Nkhani Yosiyirana: Muzitsanzira Anthu Omwe Anayembekezera Mofunitsitsa
• Habakuku
• Yohane
• Anna
11:05 Nyimbo Na. 142 ndi Zilengezo
11:15 Kodi Mukuyembekezera Chiyani?
11:30 Kudzipereka Ndiponso Kubatizidwa
12:00 Nyimbo Na. 28
Masana
1:10 Kumvetsera Nyimbo
1:20 Nyimbo Na. 54 ndi Pemphero
1:30 Nkhani ya Baibulo ya Onse: Kodi Kuleza Mtima N’kofunikabe Masiku Ano?
2:00 Phunziro Lachidule la Nsanja ya Olonda
2:30 Nyimbo Na. 143 ndi Zilengezo
2:40 Nkhani Yosiyirana: Muziyembekezera Yehova . . .
• Mukamadzimva Kuti Muli Nokhanokha
• Mukalakwitsa Zinazake
• Mukamaona Kuti Oipa Zikuwayendera Bwino
3:40 “Wolungama Adzalandira Mphoto”
4:15 Nyimbo Na. 140 ndi Pemphero