Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • wp18 No. 2 tsamba 16
  • “Anthu Ofatsa Adzalandira Dziko Lapansi”

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • “Anthu Ofatsa Adzalandira Dziko Lapansi”
  • Nsanja ya Olonda Yolengeza Ufumu wa Yehova (Yogawira)——2018
  • Nkhani Yofanana
  • Mmene Kudziwa Choonadi Kungakuthandizireni
    Nsanja ya Olonda Yolengeza Ufumu wa Yehova (Yogawira)—2020
  • Mungathe Kukhala pa Ubwenzi ndi Mulungu
    Nsanja ya Olonda Yolengeza Ufumu wa Yehova (Yogawira)—2019
  • Zomwe Mungasankhe Zingakhudze Tsogolo Lanu
    Nsanja ya Olonda Yolengeza Ufumu wa Yehova (Yogawira)—2021
  • Kodi Mukuganiza Kuti Zinthu Zidzakhala Bwanji M’tsogolo?
    Kodi Mukuganiza Kuti Zinthu Zidzakhala Bwanji M’tsogolo?
Onani Zambiri
Nsanja ya Olonda Yolengeza Ufumu wa Yehova (Yogawira)——2018
wp18 No. 2 tsamba 16
Banja

“Anthu Ofatsa Adzalandira Dziko Lapansi”

Ambirife taonapo anthu akupotoza chilungamo komanso osalakwa akuponderezedwa ndi anthu oipa. Kodi idzafika nthawi pamene sikudzakhalanso zoipa ndiponso zinthu zopanda chilungamo?

Baibulo pa Salimo 37 limapereka yankho la funsoli komanso malangizo omwe angatithandize. Taonaninso mmene Salimoli limayankhira mafunso ofunika kwambiri awa:

  • Kodi tizitani anthu ena akamatizunza?​—Vesi 1, 2.

  • Kodi n’chiyani chidzachitikire anthu oipa?​—Vesi 10.

  • Kodi anthu amene amachita zabwino ali ndi tsogolo lotani?​—Vesi 11, 29.

  • Kodi tiyenera kuchita chiyani panopa?​—Vesi 34.

Mfundo zimene zimapezeka mu Salimo 37 zimafotokoza momveka bwino zokhudza tsogolo labwino la anthu omwe ‘amayembekezera Yehova, ndi kusunga njira zake.’ A Mboni za Yehova angasangalale kwambiri kukuthandizani kuti muphunzire Baibulo komanso kuti mudziwe zimene mungachite kuti inuyo komanso anthu amene mumawakonda, mudzalandire madalitso amene Mulungu walonjeza.

Kuti mudziwe zambiri zokhudza cholinga chimene Mulungu ali nacho chokhudza anthu komanso dziko lapansili, werengani mutu 3 m’buku lakuti, Zimene Baibulo Limaphunzitsa lofalitsidwa ndi a Mboni za Yehova. Bukuli likupezekanso pa www.jw.org/ny

    Mabuku a Chichewa (1974-2025)
    Tulukani
    Lowani
    • Chichewa
    • Tumizirani Ena
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • Privacy Settings
    • JW.ORG
    • Lowani
    Tumizirani Ena