Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • wp19 No. 1 tsamba 16
  • Mungathe Kukhala pa Ubwenzi ndi Mulungu

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • Mungathe Kukhala pa Ubwenzi ndi Mulungu
  • Nsanja ya Olonda Yolengeza Ufumu wa Yehova (Yogawira)—2019
  • Nkhani Yofanana
  • “Amakuderani Nkhawa”
    Nsanja ya Olonda Yolengeza Ufumu wa Yehova (Yogawira)—2019
  • Mmene Kudziwa Choonadi Kungakuthandizireni
    Nsanja ya Olonda Yolengeza Ufumu wa Yehova (Yogawira)—2020
  • Kodi Mulungu Amamva Bwanji Akamakuonani Mukuvutika?
    Nsanja ya Olonda Yolengeza Ufumu wa Yehova (Yogawira)——2018
  • “Anthu Ofatsa Adzalandira Dziko Lapansi”
    Nsanja ya Olonda Yolengeza Ufumu wa Yehova (Yogawira)——2018
Onani Zambiri
Nsanja ya Olonda Yolengeza Ufumu wa Yehova (Yogawira)—2019
wp19 No. 1 tsamba 16

Mungathe Kukhala pa Ubwenzi ndi Mulungu

ANTHU ENA AMAONA KUTI . . .

Zimenezi n’zosatheka chifukwa Mulungu alibe nafe chidwi, ndi wapamwamba, ndi woyera kwambiri komanso si waubwenzi.

ZIMENE BAIBULO LIMANENA

Mzimayi akuwerenga Baibulo

“Yandikirani Mulungu, ndipo iyenso adzakuyandikirani.”​—Yakobo 4:8.

“[Mutulireni] nkhawa zanu zonse, pakuti amakuderani nkhawa.”​—1 Petulo 5:7.

KODI TINGATANI KUTI TIKHALE PA UBWENZI NDI MULUNGU?

  • Muzilankhula naye.​—Salimo 145:18, 19.

  • Muzimumvetsera.​—Salimo 32:8.

  • Muzitsatira malangizo ake.​—Miyambo 3:5, 6.

  • Musataye mtima.​—Mateyu 7:7, 8.

Kuti mudziwe zambiri zokhudza tsogolo labwino lomwe Mulungu watilonjeza, lolani kuti muziphunzira Baibulo pogwiritsa ntchito kabuku kakuti Mungakhale Ndi Moyo Mpaka Kalekale, komwe ndi kofalitsidwa ndi a Mboni za Yehova ndipo kakupezekanso pa www.jw.org/ny

    Mabuku a Chichewa (1974-2025)
    Tulukani
    Lowani
    • Chichewa
    • Tumizirani Ena
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • Privacy Settings
    • JW.ORG
    • Lowani
    Tumizirani Ena