Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • wp19 No. 2 tsamba 16
  • “Amakuderani Nkhawa”

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • “Amakuderani Nkhawa”
  • Nsanja ya Olonda Yolengeza Ufumu wa Yehova (Yogawira)—2019
  • Nkhani Yofanana
  • Mungathe Kukhala pa Ubwenzi ndi Mulungu
    Nsanja ya Olonda Yolengeza Ufumu wa Yehova (Yogawira)—2019
  • Mmene Kudziwa Choonadi Kungakuthandizireni
    Nsanja ya Olonda Yolengeza Ufumu wa Yehova (Yogawira)—2020
  • Kodi Mulungu Amamva Bwanji Akamakuonani Mukuvutika?
    Nsanja ya Olonda Yolengeza Ufumu wa Yehova (Yogawira)——2018
  • Kodi Mavuto Amene Tikukumana Nawowa Adzathadi?
    Kodi Mavuto Amene Tikukumana Nawowa Adzathadi?
Onani Zambiri
Nsanja ya Olonda Yolengeza Ufumu wa Yehova (Yogawira)—2019
wp19 No. 2 tsamba 16

“Amakuderani Nkhawa”

Mtsikana akuyenda akumwetulira pamene akudutsana ndi anthu ambirimbiri

Ngakhale anthu ena atakukhumudwitsani, pali wina amene sangakukhumudwitseni. Kodi ameneyu ndi ndani?

Mfumu Davide ananena kuti: “Ngakhale bambo anga ndi mayi anga atandisiya, Yehova adzanditenga.”​—Salimo 27:10.

Yehova ndi “Tate wachifundo chachikulu ndi Mulungu amene amatitonthoza m’njira iliyonse, amenenso amatitonthoza m’masautso athu onse.”​—2 Akorinto 1:3, 4.

“Muzimutulira nkhawa zanu zonse, pakuti amakuderani nkhawa.”​—1 Petulo 5:7.

Kuti mudziwe mmene Mulungu angakuthandizireni, werengani mutu 12 m’buku lakuti, Zimene Baibulo Limaphunzitsa. Bukuli ndi lofalitsidwa ndi a Mboni za Yehova ndipo likupezekanso pa www.jw.org/ny

Kuti mudziwe zimene mungachite kuti mukhale pa ubwenzi ndi Mulungu, werengani mutu 12 m’buku ili. Bukuli ndi lofalitsidwa ndi a Mboni za Yehova ndipo likupezekanso pa www.jw.org/ny

    Mabuku a Chichewa (1974-2025)
    Tulukani
    Lowani
    • Chichewa
    • Tumizirani Ena
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • Privacy Settings
    • JW.ORG
    • Lowani
    Tumizirani Ena